GULANI MALO KU DWANGWA

Dwangwa ndi dela la ndalama komanso la mtendele. Masiku ano anthu ochokela mumaboma osiyanasiyana akugula malo okhala komanso a business mu mzinda wa Dwangwa. Mu mzinda wa Dwangwa muli njira zikuluzikulu 4 zimene zimapangisa kuzungulira kwa ndalama. Njira yoyamba tili ndi DWANGWA SUGAR CORPARATION, iyi ndi company yopanga sugar

Popular Posts